Yeremiya 14:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ngakhale kuti zolakwa zathu n’zoonekeratu, inu Yehova, chitanipo kanthu chifukwa cha dzina lanu,+ pakuti zochita zathu zosonyeza kusakhulupirika zachuluka+ ndipo takuchimwirani.+ Hoseya 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kunyada kwa Isiraeli kwakhala umboni womutsutsa,+ ndipo Isiraeli ndi Efuraimu apunthwa ndi zochita zawo.+ Nayenso Yuda wapunthwa pamodzi nawo.+
7 Ngakhale kuti zolakwa zathu n’zoonekeratu, inu Yehova, chitanipo kanthu chifukwa cha dzina lanu,+ pakuti zochita zathu zosonyeza kusakhulupirika zachuluka+ ndipo takuchimwirani.+
5 Kunyada kwa Isiraeli kwakhala umboni womutsutsa,+ ndipo Isiraeli ndi Efuraimu apunthwa ndi zochita zawo.+ Nayenso Yuda wapunthwa pamodzi nawo.+