Yoswa 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Akanani ndi anthu onse a m’dziko lino adzamva zimenezi, ndipo adzatizinga ndithu, ndi kufafaniza dzina lathu kulichotsa padziko lapansi.+ Nanga zikatero mudzaliteteza bwanji dzina lanu lalikulu?”+ Salimo 25:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa cha dzina lanu, inu Yehova,+Mundikhululukire cholakwa changa ngakhale kuti n’chachikulu.+ Salimo 115:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 115 Ife sitikuyenerera kalikonse, inu Yehova, ife sitikuyenerera kalikonse,+Koma dzina lanu ndi loyenera kulemekezedwa+Malinga ndi kukoma mtima kwanu kosatha, malinganso ndi choonadi chanu.+
9 Akanani ndi anthu onse a m’dziko lino adzamva zimenezi, ndipo adzatizinga ndithu, ndi kufafaniza dzina lathu kulichotsa padziko lapansi.+ Nanga zikatero mudzaliteteza bwanji dzina lanu lalikulu?”+
11 Chifukwa cha dzina lanu, inu Yehova,+Mundikhululukire cholakwa changa ngakhale kuti n’chachikulu.+
115 Ife sitikuyenerera kalikonse, inu Yehova, ife sitikuyenerera kalikonse,+Koma dzina lanu ndi loyenera kulemekezedwa+Malinga ndi kukoma mtima kwanu kosatha, malinganso ndi choonadi chanu.+