Yobu 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye wandichotsera ulemerero wanga,+Wandilanda chisoti chaulemu cha kumutu kwanga. Salimo 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mdani wanga afunefune moyo wanga,+Ndipo aupeze ndi kuupondaponda pafumbi.Ulemerero wanga aukwirire m’fumbi. [Seʹlah.] Salimo 89:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Mwakana moipidwa pangano la mtumiki wanu.Mwanyoza chisoti chake chachifumu mwa kuchiponyera pansi.+
5 Mdani wanga afunefune moyo wanga,+Ndipo aupeze ndi kuupondaponda pafumbi.Ulemerero wanga aukwirire m’fumbi. [Seʹlah.]
39 Mwakana moipidwa pangano la mtumiki wanu.Mwanyoza chisoti chake chachifumu mwa kuchiponyera pansi.+