Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 26:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndinakutulutsani m’dziko la Iguputo kuti musakhale akapolo a Aiguputo.+ Ndinathyola goli lanu ndi kukuchititsani kuyenda mowongoka.+

  • Deuteronomo 4:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Musachite zimenezo chifukwa Yehova ndiye anakutengani n’kukutulutsani m’ng’anjo yachitsulo,+ mu Iguputo, kuti mukhale anthu akeake+ monga mmene zilili lero.

  • Yesaya 9:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Pakuti goli la katundu wawo,+ ndodo yomwe inali pamapewa awo, ndiponso ndodo ya amene anali kuwakusira ku ntchito,+ mwazithyolathyola ngati pa tsiku limene Amidiyani anagonjetsedwa.+

  • Nahumu 1:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Tsopano ndidzathyola goli lake lonyamulira katundu ndi kulichotsa pa iwe,+ ndipo ndidzadula zingwe zimene anakumanga nazo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena