Ezekieli 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chotero ine ndinalowa, ndipo ndinaona kuti pamakoma anajambulapo zithunzi+ za nyama iliyonse yokwawa, za chilombo chilichonse chonyansa+ ndi za mafano onse onyansa a nyumba ya Isiraeli.+ Pamakoma onse anajambulapo zithunzizo mochita kugoba. Ezekieli 23:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iye anawonjezera zochita zake zauhule ataona zithunzi za amuna zogoba pakhoma,+ zithunzi+ za Akasidi zopaka utoto wofiira,+
10 Chotero ine ndinalowa, ndipo ndinaona kuti pamakoma anajambulapo zithunzi+ za nyama iliyonse yokwawa, za chilombo chilichonse chonyansa+ ndi za mafano onse onyansa a nyumba ya Isiraeli.+ Pamakoma onse anajambulapo zithunzizo mochita kugoba.
14 Iye anawonjezera zochita zake zauhule ataona zithunzi za amuna zogoba pakhoma,+ zithunzi+ za Akasidi zopaka utoto wofiira,+