Yeremiya 22:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iye akunena kuti, ‘Ndimanga nyumba yaikulu ndi zipinda zikuluzikulu zam’mwamba.+ Ndikulitsa mawindo ake ndipo ndiyala matabwa a mkungudza+ ndi kupaka utoto wofiira.’+
14 Iye akunena kuti, ‘Ndimanga nyumba yaikulu ndi zipinda zikuluzikulu zam’mwamba.+ Ndikulitsa mawindo ake ndipo ndiyala matabwa a mkungudza+ ndi kupaka utoto wofiira.’+