Yesaya 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsoka kwa anthu amene akuwonjezera nyumba zina panyumba zawo,+ ndiponso amene akuwonjezera minda ina kuminda yawo, mpaka malo onse kutha,+ ndipo amuna inu mwayamba kukhala nokhanokha m’dzikoli.
8 Tsoka kwa anthu amene akuwonjezera nyumba zina panyumba zawo,+ ndiponso amene akuwonjezera minda ina kuminda yawo, mpaka malo onse kutha,+ ndipo amuna inu mwayamba kukhala nokhanokha m’dzikoli.