Ezekieli 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chotero ine ndinalowa, ndipo ndinaona kuti pamakoma anajambulapo zithunzi+ za nyama iliyonse yokwawa, za chilombo chilichonse chonyansa+ ndi za mafano onse onyansa a nyumba ya Isiraeli.+ Pamakoma onse anajambulapo zithunzizo mochita kugoba.
10 Chotero ine ndinalowa, ndipo ndinaona kuti pamakoma anajambulapo zithunzi+ za nyama iliyonse yokwawa, za chilombo chilichonse chonyansa+ ndi za mafano onse onyansa a nyumba ya Isiraeli.+ Pamakoma onse anajambulapo zithunzizo mochita kugoba.