Ezekieli 16:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Unamanga malo ako okwerawo pamphambano iliyonse ya msewu+ ndipo unaipitsa kukongola kwako.+ Unayamba kukhanyulira munthu aliyense wodutsa+ n’kumachulukitsa zochita zako zauhule.+ Ezekieli 23:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Oholiba anayamba kuchita uhule modzionetsera ndipo anali kudzivula,+ moti ine ndinasiya kukhala naye chifukwa chonyansidwa naye, monga mmene ndinasiyira mkulu wake chifukwa chonyansidwa naye.+
25 Unamanga malo ako okwerawo pamphambano iliyonse ya msewu+ ndipo unaipitsa kukongola kwako.+ Unayamba kukhanyulira munthu aliyense wodutsa+ n’kumachulukitsa zochita zako zauhule.+
18 “Oholiba anayamba kuchita uhule modzionetsera ndipo anali kudzivula,+ moti ine ndinasiya kukhala naye chifukwa chonyansidwa naye, monga mmene ndinasiyira mkulu wake chifukwa chonyansidwa naye.+