Deuteronomo 32:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yehova ataona zimenezi anayamba kuwanyoza,+Chifukwa chakuti ana ake aamuna ndi aakaziwo anam’sautsa. Salimo 78:59 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 59 Mulungu anamva+ ndipo anakwiya kwambiri.+Chotero ananyansidwa kwambiri ndi Isiraeli.+ Salimo 106:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Mkwiyo wa Yehova unayamba kuyakira anthu ake,+Ndipo iye ananyansidwa ndi cholowa chake.+ Yeremiya 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwe Yerusalemu, mvera chilango+ kuti ndisatembenuke ndi kukufulatira chifukwa chonyansidwa nawe,+ kuti ndisakusandutse bwinja, dziko lopanda munthu aliyense wokhalamo.”+ Yeremiya 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Wokondedwa wangayo, amene ndi cholowa changa, wakhala ngati mkango kwa ine m’nkhalango ndipo wandibangulira. N’chifukwa chake ndadana naye.+
19 Yehova ataona zimenezi anayamba kuwanyoza,+Chifukwa chakuti ana ake aamuna ndi aakaziwo anam’sautsa.
8 Iwe Yerusalemu, mvera chilango+ kuti ndisatembenuke ndi kukufulatira chifukwa chonyansidwa nawe,+ kuti ndisakusandutse bwinja, dziko lopanda munthu aliyense wokhalamo.”+
8 Wokondedwa wangayo, amene ndi cholowa changa, wakhala ngati mkango kwa ine m’nkhalango ndipo wandibangulira. N’chifukwa chake ndadana naye.+