Ezekieli 23:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Oholiba anayamba kuchita uhule modzionetsera ndipo anali kudzivula,+ moti ine ndinasiya kukhala naye chifukwa chonyansidwa naye, monga mmene ndinasiyira mkulu wake chifukwa chonyansidwa naye.+ Hoseya 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti ngakhale alere ana awo, ine ndidzawaphera anawo moti sadzakula n’kukhala amuna.+ Tsoka kwa iwo ndikadzawachokera!+
18 “Oholiba anayamba kuchita uhule modzionetsera ndipo anali kudzivula,+ moti ine ndinasiya kukhala naye chifukwa chonyansidwa naye, monga mmene ndinasiyira mkulu wake chifukwa chonyansidwa naye.+
12 Pakuti ngakhale alere ana awo, ine ndidzawaphera anawo moti sadzakula n’kukhala amuna.+ Tsoka kwa iwo ndikadzawachokera!+