Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 3:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Kweza maso ako ndi kuona njira zodutsidwadutsidwa.+ Ndi pamalo ati pamene amuna sanakugonerepo?+ Unali kukhala m’mbali mwa njira kudikirira okondedwa ako, ngati mmene Mluya amakhalira m’chipululu.+ Ukuipitsa dzikoli ndi zochita zako zauhule komanso kuipa kwako.+

  • Ezekieli 16:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Popeza wasonyeza chilakolako chako chonyansa mopitirira muyezo+ ndipo maliseche ako+ aonekera pamtunda pamene unali kuchita zauhule ndi zibwenzi zako+ ndi mafano ako onse onyansa,+ ndiponso chifukwa cha magazi a ana ako amene unawapereka kwa mafanowo,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena