Genesis 38:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho Yuda anapatukira kwa mkaziyo pambali pa msewu n’kumuuza kuti: “Ndikufuna ndigone nawe.”+ Anatero posadziwa kuti anali mpongozi wake.+ Koma mkaziyo anayankha kuti: “Mundipatsa chiyani kuti mugone nane?”+ Miyambo 23:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndithudi iye mofanana ndi wachifwamba,+ amabisalira anthu panjira, ndipo amachulukitsa amuna achinyengo.+
16 Choncho Yuda anapatukira kwa mkaziyo pambali pa msewu n’kumuuza kuti: “Ndikufuna ndigone nawe.”+ Anatero posadziwa kuti anali mpongozi wake.+ Koma mkaziyo anayankha kuti: “Mundipatsa chiyani kuti mugone nane?”+
28 Ndithudi iye mofanana ndi wachifwamba,+ amabisalira anthu panjira, ndipo amachulukitsa amuna achinyengo.+