Numeri 25:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Tsopano Aisiraeli anali kukhala ku Sitimu.+ Ali kumeneko, iwo anayamba kuchita chiwerewere ndi akazi a ku Mowabu.+ 1 Akorinto 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tisamachite dama,+ mmene ena mwa iwo anachitira dama, n’kufa 23,000 tsiku limodzi.+
25 Tsopano Aisiraeli anali kukhala ku Sitimu.+ Ali kumeneko, iwo anayamba kuchita chiwerewere ndi akazi a ku Mowabu.+