1 Mafumu 15:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho iye anachotsa mahule aamuna a pakachisi m’dzikolo,+ ndiponso mafano onse onyansa*+ amene makolo ake anapanga.+ 2 Mafumu 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anapitiriza kutumikira mafano onyansa.*+ Ponena za mafano amenewa, Yehova anawauza kuti: “Musachite zimenezi.”+ 2 Mafumu 21:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Manase+ mfumu ya Yuda yachita zinthu zonyansazi.+ Yachita zinthu zoipa kwambiri kuposa zonse zimene anachita Aamori+ amene analiko iye asanakhale mfumu. Iye wachimwitsa ngakhale Yuda+ ndi mafano ake onyansa.
12 Choncho iye anachotsa mahule aamuna a pakachisi m’dzikolo,+ ndiponso mafano onse onyansa*+ amene makolo ake anapanga.+
12 Anapitiriza kutumikira mafano onyansa.*+ Ponena za mafano amenewa, Yehova anawauza kuti: “Musachite zimenezi.”+
11 “Manase+ mfumu ya Yuda yachita zinthu zonyansazi.+ Yachita zinthu zoipa kwambiri kuposa zonse zimene anachita Aamori+ amene analiko iye asanakhale mfumu. Iye wachimwitsa ngakhale Yuda+ ndi mafano ake onyansa.