Ekisodo 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Usakhale ndi milungu ina iliyonse+ kupatulapo ine.* Levitiko 26:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “‘Musadzipangire milungu yopanda pake,+ chifaniziro,+ kapena chipilala chopatulika. Musaike mwala wokhala ndi zithunzi zojambula mochita kugoba+ m’dziko lanu kuti muziugwadira,+ chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wanu. Deuteronomo 4:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Samalani kuti musaiwale pangano la Yehova Mulungu wanu limene anachita nanu,+ ndi kuti musadzipangire chifaniziro, chifaniziro cha chinthu chilichonse chimene Yehova Mulungu wanu anakuletsani.+
26 “‘Musadzipangire milungu yopanda pake,+ chifaniziro,+ kapena chipilala chopatulika. Musaike mwala wokhala ndi zithunzi zojambula mochita kugoba+ m’dziko lanu kuti muziugwadira,+ chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wanu.
23 Samalani kuti musaiwale pangano la Yehova Mulungu wanu limene anachita nanu,+ ndi kuti musadzipangire chifaniziro, chifaniziro cha chinthu chilichonse chimene Yehova Mulungu wanu anakuletsani.+