Deuteronomo 23:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Mwana wamkazi aliyense wachiisiraeli asakhale hule wa pakachisi,+ ndiponso mwana wamwamuna aliyense wachiisiraeli asakhale hule wa pakachisi.*+ 1 Mafumu 14:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ngakhalenso mahule aamuna a pakachisi ankapezeka m’dzikomo.+ Anthuwo anachita zinthu zonse zonyansa zimene inkachita mitundu imene Yehova anaithamangitsa pamaso pa ana a Isiraeli.+ 1 Mafumu 22:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Mahule aamuna a pakachisi+ amene anatsalira m’masiku a Asa bambo ake, Yehosafati anawachotsa m’dzikolo.+ 1 Akorinto 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi zoonadi inu simukudziwa kuti anthu osalungama sadzalowa mu ufumu wa Mulungu?+ Musasocheretsedwe. Adama,+ opembedza mafano,+ achigololo,+ amuna amene amagonedwa ndi amuna anzawo,+ amuna ogona amuna anzawo,+
17 “Mwana wamkazi aliyense wachiisiraeli asakhale hule wa pakachisi,+ ndiponso mwana wamwamuna aliyense wachiisiraeli asakhale hule wa pakachisi.*+
24 Ngakhalenso mahule aamuna a pakachisi ankapezeka m’dzikomo.+ Anthuwo anachita zinthu zonse zonyansa zimene inkachita mitundu imene Yehova anaithamangitsa pamaso pa ana a Isiraeli.+
46 Mahule aamuna a pakachisi+ amene anatsalira m’masiku a Asa bambo ake, Yehosafati anawachotsa m’dzikolo.+
9 Kodi zoonadi inu simukudziwa kuti anthu osalungama sadzalowa mu ufumu wa Mulungu?+ Musasocheretsedwe. Adama,+ opembedza mafano,+ achigololo,+ amuna amene amagonedwa ndi amuna anzawo,+ amuna ogona amuna anzawo,+