Levitiko 19:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “‘Musaipitse mwana wanu wamkazi mwa kum’sandutsa hule,+ kuti dziko lingachite uhule ndi kudzaza makhalidwe otayirira.+ Levitiko 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “‘Mwana wamkazi wa wansembe akadziipitsa mwa kuchita uhule, pamenepo waipitsa bambo ake. Aziphedwa ndi kutenthedwa.+
29 “‘Musaipitse mwana wanu wamkazi mwa kum’sandutsa hule,+ kuti dziko lingachite uhule ndi kudzaza makhalidwe otayirira.+
9 “‘Mwana wamkazi wa wansembe akadziipitsa mwa kuchita uhule, pamenepo waipitsa bambo ake. Aziphedwa ndi kutenthedwa.+