Deuteronomo 23:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Mwana wamkazi aliyense wachiisiraeli asakhale hule wa pakachisi,+ ndiponso mwana wamwamuna aliyense wachiisiraeli asakhale hule wa pakachisi.*+ 1 Mafumu 15:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho iye anachotsa mahule aamuna a pakachisi m’dzikolo,+ ndiponso mafano onse onyansa*+ amene makolo ake anapanga.+ 1 Mafumu 22:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Mahule aamuna a pakachisi+ amene anatsalira m’masiku a Asa bambo ake, Yehosafati anawachotsa m’dzikolo.+
17 “Mwana wamkazi aliyense wachiisiraeli asakhale hule wa pakachisi,+ ndiponso mwana wamwamuna aliyense wachiisiraeli asakhale hule wa pakachisi.*+
12 Choncho iye anachotsa mahule aamuna a pakachisi m’dzikolo,+ ndiponso mafano onse onyansa*+ amene makolo ake anapanga.+
46 Mahule aamuna a pakachisi+ amene anatsalira m’masiku a Asa bambo ake, Yehosafati anawachotsa m’dzikolo.+