Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 20:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 “‘Mwamuna akagona ndi mwamuna mnzake, mmene mwamuna amagonera ndi mkazi, onse awiri achita chinthu chonyansa.+ Iwo aziphedwa ndithu. Mlandu wa magazi awo ukhale wa iwo eni.

  • Aroma 1:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Amunanso chimodzimodzi. Iwo anasiya njira yachibadwa yofuna akazi+ n’kumatenthetsana okhaokha mwachiwawa m’chilakolako choipa, amuna ndi amuna anzawo,+ kuchitirana zonyansa+ ndi kulandiriratu mphoto+ yoyenerera kulakwa kwawo.+

  • 1 Akorinto 6:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Kodi zoonadi inu simukudziwa kuti anthu osalungama sadzalowa mu ufumu wa Mulungu?+ Musasocheretsedwe. Adama,+ opembedza mafano,+ achigololo,+ amuna amene amagonedwa ndi amuna anzawo,+ amuna ogona amuna anzawo,+

  • 1 Timoteyo 1:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 adama,+ amuna ogonana ndi amuna anzawo, oba anthu, onama, olumbira monama,+ ndiponso ochita china chilichonse chosagwirizana+ ndi chiphunzitso cholondola.+

  • Yuda 7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Komanso mizinda ya Sodomu ndi Gomora ndi mizinda yozungulira mizinda imeneyi,+ inalandira chilango cha moto wosatha,+ motero yaikidwa monga chitsanzo chotichenjeza.+ Anthu ake anachita mofanana ndi amene tatchula aja, pochita dama loipitsitsa ndiponso pogonana m’njira imene si yachibadwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena