1 Mafumu 14:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ngakhalenso mahule aamuna a pakachisi ankapezeka m’dzikomo.+ Anthuwo anachita zinthu zonse zonyansa zimene inkachita mitundu imene Yehova anaithamangitsa pamaso pa ana a Isiraeli.+ 1 Mafumu 15:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho iye anachotsa mahule aamuna a pakachisi m’dzikolo,+ ndiponso mafano onse onyansa*+ amene makolo ake anapanga.+ 2 Mafumu 23:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inagwetsanso nyumba za mahule achimuna a pakachisi+ zimene zinali m’nyumba ya Yehova, mmene akazi anali kulukiramo akachisi a mahema a mzati wopatulika.
24 Ngakhalenso mahule aamuna a pakachisi ankapezeka m’dzikomo.+ Anthuwo anachita zinthu zonse zonyansa zimene inkachita mitundu imene Yehova anaithamangitsa pamaso pa ana a Isiraeli.+
12 Choncho iye anachotsa mahule aamuna a pakachisi m’dzikolo,+ ndiponso mafano onse onyansa*+ amene makolo ake anapanga.+
7 Inagwetsanso nyumba za mahule achimuna a pakachisi+ zimene zinali m’nyumba ya Yehova, mmene akazi anali kulukiramo akachisi a mahema a mzati wopatulika.