Salimo 106:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Choncho anali kukhetsa magazi a anthu osalakwa,+Magazi a ana awo aamuna ndi a ana awo aakazi,Amene anawapereka nsembe kwa mafano a ku Kanani.+Ndipo dzikolo linaipa ndi magazi amene iwo anakhetsa.+ Yeremiya 2:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Komanso, pazovala zako papezeka madontho a magazi a anthu+ osauka osalakwa.+ Madontho a magaziwo sindinawapeze panyumba, ngati kuti anali kuthyola nyumbayo, koma ndawapeza pazovala zako zonse.+
38 Choncho anali kukhetsa magazi a anthu osalakwa,+Magazi a ana awo aamuna ndi a ana awo aakazi,Amene anawapereka nsembe kwa mafano a ku Kanani.+Ndipo dzikolo linaipa ndi magazi amene iwo anakhetsa.+
34 Komanso, pazovala zako papezeka madontho a magazi a anthu+ osauka osalakwa.+ Madontho a magaziwo sindinawapeze panyumba, ngati kuti anali kuthyola nyumbayo, koma ndawapeza pazovala zako zonse.+