Maliro 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Zovala+ zake ndi zodetsedwa. Iye sanaganizire za tsogolo+ lake.Wagwa modabwitsa ndipo alibe womutonthoza.+Inu Yehova, onani kusautsika+ kwanga, pakuti mdani wanga akudzitukumula.+
9 Zovala+ zake ndi zodetsedwa. Iye sanaganizire za tsogolo+ lake.Wagwa modabwitsa ndipo alibe womutonthoza.+Inu Yehova, onani kusautsika+ kwanga, pakuti mdani wanga akudzitukumula.+