Deuteronomo 9:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Iwo ndi anthu anube, chuma chanu chapadera,+ anthu amene munawatulutsa ndi mphamvu zanu zazikulu ndi dzanja lanu lotambasula.’+ Deuteronomo 32:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yehova ataona zimenezi anayamba kuwanyoza,+Chifukwa chakuti ana ake aamuna ndi aakaziwo anam’sautsa.
29 Iwo ndi anthu anube, chuma chanu chapadera,+ anthu amene munawatulutsa ndi mphamvu zanu zazikulu ndi dzanja lanu lotambasula.’+
19 Yehova ataona zimenezi anayamba kuwanyoza,+Chifukwa chakuti ana ake aamuna ndi aakaziwo anam’sautsa.