Oweruza 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pamenepo mkwiyo wa Yehova unayakira Isiraeli,+ moti anawapereka m’manja mwa ofunkha, ndipo anayamba kufunkha zinthu zawo.+ Iye anawagulitsa kwa adani awo owazungulira+ moti sanathe kuima pamaso pa adani awo.+ Salimo 78:59 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 59 Mulungu anamva+ ndipo anakwiya kwambiri.+Chotero ananyansidwa kwambiri ndi Isiraeli.+ Salimo 106:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Mkwiyo wa Yehova unayamba kuyakira anthu ake,+Ndipo iye ananyansidwa ndi cholowa chake.+
14 Pamenepo mkwiyo wa Yehova unayakira Isiraeli,+ moti anawapereka m’manja mwa ofunkha, ndipo anayamba kufunkha zinthu zawo.+ Iye anawagulitsa kwa adani awo owazungulira+ moti sanathe kuima pamaso pa adani awo.+