Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 4:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Musachite zimenezo chifukwa Yehova ndiye anakutengani n’kukutulutsani m’ng’anjo yachitsulo,+ mu Iguputo, kuti mukhale anthu akeake+ monga mmene zilili lero.

  • 1 Mafumu 8:51
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 51 (popeza iwo ndi anthu anu ndi cholowa chanu,+ amene munawatulutsa ku Iguputo,+ kuwachotsa m’ng’anjo yachitsulo).+

  • Nehemiya 1:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Iwo ndi atumiki anu+ ndi anthu anu,+ amene munawawombola ndi mphamvu zanu zazikulu+ ndi dzanja lanu lamphamvu.+

  • Salimo 74:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Kumbukirani anthu amene munawatenga kukhala anu kalelo,+

      Fuko limene munaliwombola monga cholowa chanu,+

      Ndi phiri la Ziyoni ili mmene inu mukukhala.+

  • Salimo 95:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Pakuti iye ndi Mulungu wathu ndipo ife ndife anthu ake. Iye amatisamalira ngati nkhosa zimene akuweta.+

      Lero anthu inu mukamvera mawu a Mulungu,+

  • Salimo 100:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Dziwani kuti Yehova ndi Mulungu.+

      Iye ndi amene anatipanga, sitinadzipange tokha.+

      Ndife anthu ake ndi nkhosa zimene akuweta.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena