Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 4:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Musachite zimenezo chifukwa Yehova ndiye anakutengani n’kukutulutsani m’ng’anjo yachitsulo,+ mu Iguputo, kuti mukhale anthu akeake+ monga mmene zilili lero.

  • Deuteronomo 32:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Pakuti gawo la Yehova ndilo anthu ake.+

      Yakobo ndiye gawo la cholowa chake.+

  • Salimo 33:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Wodala ndi mtundu umene Mulungu wawo ndi Yehova,+

      Anthu amene iye wawasankha kukhala cholowa chake.+

  • Yeremiya 10:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Koma Mulungu wa Yakobo+ sali ngati mafanowa. Iye ndi amene anapanga china chilichonse.+ Isiraeli ndiye ndodo ya cholowa chake.+ Dzina la Mulunguyo ndi Yehova wa makamu.+

  • Mika 7:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Weta anthu ako ndi ndodo yako.+ Weta gulu la nkhosa zomwe ndi cholowa chako, zimene zinali kukhala zokhazokha m’nkhalango pakati pa mitengo ya zipatso.+ Uzilole kuti zikadyere ku Basana ndi ku Giliyadi+ ngati mmene zinali kuchitira masiku akale.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena