Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 28:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “Mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu ndi kuonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi mfundo zake zimene ndikukupatsani lero, matemberero otsatirawa adzakugwerani ndi kukupezani:+

  • Oweruza 2:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndipo inu musachite pangano ndi anthu okhala m’dziko ili,+ m’malomwake mugwetse maguwa awo ansembe.’+ Koma inu simunamvere mawu anga.+ N’chifukwa chiyani mwachita zimenezi?+

  • Yeremiya 3:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Koma ganizirani zolakwa zanu chifukwa mwaphwanya malamulo a Yehova Mulungu wanu.+ Anthu inu simunamvere mawu anga, koma munapitiriza kupanga njira zambirimbiri zopita kwa anthu achilendo+ pansi pa mtengo uliwonse waukulu wa masamba ambiri obiriwira,”+ watero Yehova.’”

  • Zefaniya 3:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Mzindawo sunafune kumvera,+ sunalole kulangizidwa,*+ sunakhulupirire Yehova+ ndipo sunayandikire Mulungu wake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena