Deuteronomo 28:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu ndi kuonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi mfundo zake zimene ndikukupatsani lero, matemberero otsatirawa adzakugwerani ndi kukupezani:+ Yeremiya 22:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndinalankhula nawe pamene unali pa ufulu,+ koma iwe unandiyankha kuti, ‘Sindidzamvera.’+ Wakhala ukuchita zimenezi kuyambira uli wachinyamata, moti sunamvere mawu anga.+ Yeremiya 32:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iwo analowa m’dzikoli ndi kulitenga kukhala lawo,+ koma sanamvere mawu anu ndi kuyenda motsatira malamulo anu.+ Zinthu zonse zimene munawalamula kuti achite sanachite,+ chotero mwawagwetsera masoka onsewa.+
15 “Mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu ndi kuonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi mfundo zake zimene ndikukupatsani lero, matemberero otsatirawa adzakugwerani ndi kukupezani:+
21 Ndinalankhula nawe pamene unali pa ufulu,+ koma iwe unandiyankha kuti, ‘Sindidzamvera.’+ Wakhala ukuchita zimenezi kuyambira uli wachinyamata, moti sunamvere mawu anga.+
23 Iwo analowa m’dzikoli ndi kulitenga kukhala lawo,+ koma sanamvere mawu anu ndi kuyenda motsatira malamulo anu.+ Zinthu zonse zimene munawalamula kuti achite sanachite,+ chotero mwawagwetsera masoka onsewa.+