Yeremiya 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Samala kuti phazi lako lisakhale lopanda nsapato, ndi kuti usachite ludzu.+ Koma iwe unati, ‘Zimenezo ayi!+ Ine ndakondana ndi alendo+ ndipo ndidzawatsatira.’+ Ezekieli 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “‘Koma unayamba kudalira kukongola kwako+ ndipo unakhala hule chifukwa cha kutchuka kwa dzina lako.+ Unayamba kuchita uhule mosadziletsa ndi munthu aliyense wodutsa m’njira.+ Kukongola kwako unakupereka kwa anthu odutsawo.
25 Samala kuti phazi lako lisakhale lopanda nsapato, ndi kuti usachite ludzu.+ Koma iwe unati, ‘Zimenezo ayi!+ Ine ndakondana ndi alendo+ ndipo ndidzawatsatira.’+
15 “‘Koma unayamba kudalira kukongola kwako+ ndipo unakhala hule chifukwa cha kutchuka kwa dzina lako.+ Unayamba kuchita uhule mosadziletsa ndi munthu aliyense wodutsa m’njira.+ Kukongola kwako unakupereka kwa anthu odutsawo.