Hoseya 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 kuti ndisamuvule ndi kumukhalitsa wamaliseche+ ngati tsiku limene anabadwa,+ kutinso ndisamuchititse kukhala ngati chipululu+ ndi dziko lopanda madzi+ ndiponso kuti ndisamuphe ndi ludzu.+
3 kuti ndisamuvule ndi kumukhalitsa wamaliseche+ ngati tsiku limene anabadwa,+ kutinso ndisamuchititse kukhala ngati chipululu+ ndi dziko lopanda madzi+ ndiponso kuti ndisamuphe ndi ludzu.+