Oweruza 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno anamva ludzu koopsa, ndipo anayamba kufuulira Yehova kuti: “Ndinu amene mwapereka chipulumutso chachikulu chimenechi m’manja mwa mtumiki wanu.+ Tsopano kodi ndife ndi ludzu, ndigwere m’manja mwa anthu osadulidwa?”+
18 Ndiyeno anamva ludzu koopsa, ndipo anayamba kufuulira Yehova kuti: “Ndinu amene mwapereka chipulumutso chachikulu chimenechi m’manja mwa mtumiki wanu.+ Tsopano kodi ndife ndi ludzu, ndigwere m’manja mwa anthu osadulidwa?”+