Salimo 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nyamukani,+ inu Yehova! Ndipulumutseni+ inu Mulungu wanga!+Pakuti mudzakantha adani anga onse pachibwano.+Mano a anthu oipa mudzawaphwanyaphwanya.+ Salimo 18:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kodi pali Mulungu winanso woposa Yehova?+Kodi pali thanthwe linanso loposa Mulungu wathu?+ Salimo 44:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti iwo sanatenge dzikolo chifukwa cha lupanga lawo,+Ndipo si mkono wawo umene unawabweretsera chipulumutso.+Koma chinabwera ndi dzanja lanu lamanja,+ mkono wanu ndi kuwala kwa nkhope yanu,Chifukwa munakondwera nawo.+
7 Nyamukani,+ inu Yehova! Ndipulumutseni+ inu Mulungu wanga!+Pakuti mudzakantha adani anga onse pachibwano.+Mano a anthu oipa mudzawaphwanyaphwanya.+
3 Pakuti iwo sanatenge dzikolo chifukwa cha lupanga lawo,+Ndipo si mkono wawo umene unawabweretsera chipulumutso.+Koma chinabwera ndi dzanja lanu lamanja,+ mkono wanu ndi kuwala kwa nkhope yanu,Chifukwa munakondwera nawo.+