Yesaya 33:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Dzikolo likulira, lafota.+ Lebanoni wachita manyazi, wanyala.+ Sharoni+ wakhala ngati chipululu ndipo Basana ndi Karimeli akuyoyola masamba awo.+ Ezekieli 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano mtengo wa mpesawo wabzalidwa m’chipululu,+ m’dziko lopanda madzi ndi louma.+
9 Dzikolo likulira, lafota.+ Lebanoni wachita manyazi, wanyala.+ Sharoni+ wakhala ngati chipululu ndipo Basana ndi Karimeli akuyoyola masamba awo.+