Yeremiya 51:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Mizinda yake yakhala chinthu chodabwitsa, dziko lopanda madzi komanso chipululu.+ Mizindayo yakhala ngati dziko limene simukukhala munthu aliyense ndipo sipadzapezeka mwana aliyense wa munthu wodutsa mmenemo.+
43 Mizinda yake yakhala chinthu chodabwitsa, dziko lopanda madzi komanso chipululu.+ Mizindayo yakhala ngati dziko limene simukukhala munthu aliyense ndipo sipadzapezeka mwana aliyense wa munthu wodutsa mmenemo.+