-
2 Mafumu 8:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Ndiyeno mfumuyo inapempha mayiyo kuti aifotokozere nkhani yonse,+ ndipo mayiyo anafotokozadi. Kenako mfumuyo inauza nduna ya panyumba yake+ kuti: “Mayiyu um’bwezere zinthu zake zonse, ndipo umupatse ndalama zimene akanapeza pa zokolola za kumunda kwake pa nthawi yonse imene anachokapo kufikira lero.”+
-