2 Mafumu 4:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Koma woperekera chakudyayo anati: “Ndingagawire bwanji chakudya chimenechi anthu 100?”+ Elisa ananena kuti: “Gawira anthuwa kuti adye, pakuti Yehova wanena kuti, ‘Anthuwa adya mokwanira chakudyachi, ndipo chitsala.’”+ Esitere 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno atumiki a mfumu, amene anali nduna zake,+ anati: “Pakhale anthu oti afufuzire+ mfumu atsikana, anamwali+ okongola.
43 Koma woperekera chakudyayo anati: “Ndingagawire bwanji chakudya chimenechi anthu 100?”+ Elisa ananena kuti: “Gawira anthuwa kuti adye, pakuti Yehova wanena kuti, ‘Anthuwa adya mokwanira chakudyachi, ndipo chitsala.’”+
2 Ndiyeno atumiki a mfumu, amene anali nduna zake,+ anati: “Pakhale anthu oti afufuzire+ mfumu atsikana, anamwali+ okongola.