Mateyu 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iwo anamuuza kuti: “Tilibe chilichonse pano, koma mitanda isanu ya mkate ndi nsomba ziwiri zokha basi.”+ Maliko 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo ophunzira ake anamuyankha kuti: “Munthu angaipeze kuti mitanda ya mkate yokwanira kudyetsa anthu onsewa kutchire ngati kuno?”+
17 Iwo anamuuza kuti: “Tilibe chilichonse pano, koma mitanda isanu ya mkate ndi nsomba ziwiri zokha basi.”+
4 Pamenepo ophunzira ake anamuyankha kuti: “Munthu angaipeze kuti mitanda ya mkate yokwanira kudyetsa anthu onsewa kutchire ngati kuno?”+