Luka 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma iye anawayankha kuti: “Inuyo muwapatse chakudya.”+ Iwo anati: “Tilibe chilichonse kuno koma mitanda ya mkate isanu ndi nsomba+ ziwiri zokha basi. Mwina tingapite kukagula chakudya chokwanira anthu onsewa.”+ Yohane 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Pali kamnyamata pano kamene kali ndi mitanda isanu ya mkate wa balere+ ndi tinsomba tiwiri. Koma nanga zimenezi zingakwanire, poyerekeza ndi chikhamu chonse cha anthuchi?”+
13 Koma iye anawayankha kuti: “Inuyo muwapatse chakudya.”+ Iwo anati: “Tilibe chilichonse kuno koma mitanda ya mkate isanu ndi nsomba+ ziwiri zokha basi. Mwina tingapite kukagula chakudya chokwanira anthu onsewa.”+
9 “Pali kamnyamata pano kamene kali ndi mitanda isanu ya mkate wa balere+ ndi tinsomba tiwiri. Koma nanga zimenezi zingakwanire, poyerekeza ndi chikhamu chonse cha anthuchi?”+