Mateyu 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iwo anamuuza kuti: “Tilibe chilichonse pano, koma mitanda isanu ya mkate ndi nsomba ziwiri zokha basi.”+ Maliko 6:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Powayankha iye anawafunsa kuti: “Muli ndi mitanda ingati ya mkate? Pitani mukaone!” Ataiona anati: “Ilipo isanu, ndi nsomba ziwiri.”+ Yohane 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Pali kamnyamata pano kamene kali ndi mitanda isanu ya mkate wa balere+ ndi tinsomba tiwiri. Koma nanga zimenezi zingakwanire, poyerekeza ndi chikhamu chonse cha anthuchi?”+
17 Iwo anamuuza kuti: “Tilibe chilichonse pano, koma mitanda isanu ya mkate ndi nsomba ziwiri zokha basi.”+
38 Powayankha iye anawafunsa kuti: “Muli ndi mitanda ingati ya mkate? Pitani mukaone!” Ataiona anati: “Ilipo isanu, ndi nsomba ziwiri.”+
9 “Pali kamnyamata pano kamene kali ndi mitanda isanu ya mkate wa balere+ ndi tinsomba tiwiri. Koma nanga zimenezi zingakwanire, poyerekeza ndi chikhamu chonse cha anthuchi?”+