Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 11:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Koma Mose anati: “Amuna amene ndikuyenda nawo akukwana 600,000,+ koma inuyo mukunena kuti, ‘Nyamayo ndiwapatsa, ndipo adzaidya kwa mwezi wonse wathunthu.’

  • 2 Mafumu 7:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Koma msilikali wothandiza mfumu amene anaigwira ndi dzanja lake,+ anayankha munthu wa Mulungu woonayo, kuti: “Ngakhale Yehova atatsegula zotsekera madzi akumwamba,+ kodi zimenezo zingachitike?”+ Pamenepo Elisa anati: “Uona zimenezi ndi maso ako,+ koma sudya nawo.”+

  • Mateyu 15:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Koma ophunzirawo anamuuza kuti: “Kopanda anthu ngati kuno tiipeza kuti mitanda ya mkate yokwanira khamu lonseli?”+

  • Maliko 6:52
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 52 Popeza sanamvetse tanthauzo la mitanda ya mkate ija, mitima yawo inakhalabe yosazindikira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena