Numeri 14:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno Yehova analankhula ndi Mose kuti: “Kodi anthu awa apitiriza kundinyoza kufikira liti?+ Kodi adzayamba liti kundikhulupirira pambuyo pa zizindikiro zonse zimene ndachita pakati pawo?+ 2 Atesalonika 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Muzitero kutinso tilanditsidwe kwa anthu opweteka anzawo ndi oipa,+ pakuti chikhulupiriro sichikhala ndi anthu onse.+
11 Ndiyeno Yehova analankhula ndi Mose kuti: “Kodi anthu awa apitiriza kundinyoza kufikira liti?+ Kodi adzayamba liti kundikhulupirira pambuyo pa zizindikiro zonse zimene ndachita pakati pawo?+
2 Muzitero kutinso tilanditsidwe kwa anthu opweteka anzawo ndi oipa,+ pakuti chikhulupiriro sichikhala ndi anthu onse.+