Mateyu 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi mfundo yake simukuimvetsabe? Kapena kodi simukukumbukira anthu 5,000 amene anadya mitanda isanu ya mkate, komanso kuchuluka kwa madengu a zotsalira zimene munatolera?+ Maliko 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamenepo Yesu anawayang’ana mokwiya ndi kumva chisoni kwambiri chifukwa cha kuuma mtima kwawo.+ Kenako anauza munthuyo kuti: “Tambasula dzanja lako.” Iye analitambasuladi, ndipo linakhala labwinobwino.+ Maliko 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yesu poona zimenezo, anawafunsa kuti: “N’chifukwa chiyani mukukangana nkhani yosowa mikate?+ Kodi simukuzindikira ndi kumvetsa tanthauzo lake mpaka pano? Kodi mitima yanu ikadali yosazindikira?+
9 Kodi mfundo yake simukuimvetsabe? Kapena kodi simukukumbukira anthu 5,000 amene anadya mitanda isanu ya mkate, komanso kuchuluka kwa madengu a zotsalira zimene munatolera?+
5 Pamenepo Yesu anawayang’ana mokwiya ndi kumva chisoni kwambiri chifukwa cha kuuma mtima kwawo.+ Kenako anauza munthuyo kuti: “Tambasula dzanja lako.” Iye analitambasuladi, ndipo linakhala labwinobwino.+
17 Yesu poona zimenezo, anawafunsa kuti: “N’chifukwa chiyani mukukangana nkhani yosowa mikate?+ Kodi simukuzindikira ndi kumvetsa tanthauzo lake mpaka pano? Kodi mitima yanu ikadali yosazindikira?+