Mateyu 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iwo anamuuza kuti: “Tilibe chilichonse pano, koma mitanda isanu ya mkate ndi nsomba ziwiri zokha basi.”+ Maliko 8:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 kuchuluka kwa madengu a zotsala zimene munatolera, pamene ndinanyemanyema mitanda isanu ya mkate+ koma n’kukwanira amuna 5,000?” Iwo anayankha kuti: “Anali madengu 12.”+
17 Iwo anamuuza kuti: “Tilibe chilichonse pano, koma mitanda isanu ya mkate ndi nsomba ziwiri zokha basi.”+
19 kuchuluka kwa madengu a zotsala zimene munatolera, pamene ndinanyemanyema mitanda isanu ya mkate+ koma n’kukwanira amuna 5,000?” Iwo anayankha kuti: “Anali madengu 12.”+