2 Mafumu 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mfumu inaika msilikali woithandiza amene anaigwira+ ndi dzanja uja kuti akhale woyang’anira pachipata. Koma anthu anam’pondaponda+ pachipatapo moti anafa, monga mmene munthu wa Mulungu woona uja ananenera,+ pamene mfumu inabwera kwa iye.
17 Mfumu inaika msilikali woithandiza amene anaigwira+ ndi dzanja uja kuti akhale woyang’anira pachipata. Koma anthu anam’pondaponda+ pachipatapo moti anafa, monga mmene munthu wa Mulungu woona uja ananenera,+ pamene mfumu inabwera kwa iye.