Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 9:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Ndiyeno Yehu anati: “M’ponyeni+ pansi Yezebeliyo!” Iwo anam’ponyadi pansi, ndipo magazi ake ena anamwazika n’kuwaza khoma ndi mahatchi. Kenako Yehu anam’pondaponda+ ndi mahatchi ake.

  • Yesaya 25:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pakuti dzanja la Yehova lidzakhazikika paphiri limeneli,+ ndipo Mowabu adzapondedwapondedwa+ pamalo pake ngati mulu wa udzu umene umapondedwapondedwa pamalo opangira manyowa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena