Salimo 83:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo anawonongedwa ku Eni-dori.+Anasanduka manyowa a m’nthaka.+ Luka 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Wosamalira mundayo anayankha kuti, ‘Mbuyanga, bwanji muusiye+ chaka chino chokha. Ine ndikumba mouzungulira n’kuthirapo manyowa.
8 Wosamalira mundayo anayankha kuti, ‘Mbuyanga, bwanji muusiye+ chaka chino chokha. Ine ndikumba mouzungulira n’kuthirapo manyowa.