2 Mafumu 9:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Ndipo mtembo wa Yezebeli, ndithu udzasanduka manyowa+ m’munda wa ku Yezereeli kuti anthu asadzanene kuti: “Uyu ndi Yezebeli.”’”+ Zefaniya 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamenepo ndidzasautsa mtundu wa anthu moti adzayenda ngati anthu akhungu+ chifukwa chakuti iwo achimwira Yehova.+ Magazi awo adzakhuthulidwa pansi ngati fumbi,+ ndipo matumbo awo adzakhuthulidwa pansi ngati ndowe.+
37 Ndipo mtembo wa Yezebeli, ndithu udzasanduka manyowa+ m’munda wa ku Yezereeli kuti anthu asadzanene kuti: “Uyu ndi Yezebeli.”’”+
17 Pamenepo ndidzasautsa mtundu wa anthu moti adzayenda ngati anthu akhungu+ chifukwa chakuti iwo achimwira Yehova.+ Magazi awo adzakhuthulidwa pansi ngati fumbi,+ ndipo matumbo awo adzakhuthulidwa pansi ngati ndowe.+