Esitere 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pa tsiku la 7, pamene mtima wa mfumu unali kukondwera ndi vinyo,+ mfumu inauza Mehumani, Bizita, Haribona,+ Bigita, Abagata, Zetara ndi Karikasi, nduna 7 za panyumba ya mfumu zimene zinali kutumikira+ Mfumu Ahasiwero, Esitere 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Alangizi amene anali pafupi kwambiri ndi mfumu anali Karisena, Setara, Adimata, Tarisi, Meresi, Marisena ndi Memukani, akalonga 7+ a Perisiya ndi Mediya, amene nthawi zonse anali kufika pamaso pa mfumu+ komanso anali ndi maudindo akuluakulu mu ufumuwo.) Esitere 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pamene anali kukambirana naye zimenezi, nduna za panyumba ya mfumu zinafika, ndipo mofulumira+ zinatenga Hamani ndi kupita naye kuphwando+ limene Esitere anakonza.
10 Pa tsiku la 7, pamene mtima wa mfumu unali kukondwera ndi vinyo,+ mfumu inauza Mehumani, Bizita, Haribona,+ Bigita, Abagata, Zetara ndi Karikasi, nduna 7 za panyumba ya mfumu zimene zinali kutumikira+ Mfumu Ahasiwero,
14 Alangizi amene anali pafupi kwambiri ndi mfumu anali Karisena, Setara, Adimata, Tarisi, Meresi, Marisena ndi Memukani, akalonga 7+ a Perisiya ndi Mediya, amene nthawi zonse anali kufika pamaso pa mfumu+ komanso anali ndi maudindo akuluakulu mu ufumuwo.)
14 Pamene anali kukambirana naye zimenezi, nduna za panyumba ya mfumu zinafika, ndipo mofulumira+ zinatenga Hamani ndi kupita naye kuphwando+ limene Esitere anakonza.