Esitere 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno mfumu inati: “Amuna inu, itanani Hamani mofulumira+ mogwirizana ndi mawu a Esitere.” Kenako mfumu ndi Hamani anafika kuphwando limene Esitere anakonza.
5 Ndiyeno mfumu inati: “Amuna inu, itanani Hamani mofulumira+ mogwirizana ndi mawu a Esitere.” Kenako mfumu ndi Hamani anafika kuphwando limene Esitere anakonza.